Anthu okhala m'mudzi wa Chikho, Mfumu yayikulu Kasakula m'boma la Ntchisi adanduala za vuto la madzi lomwe lakula m'mudziwu. Mudzi wa Chikho mulibe dilawo komanso ...
Chipwilikiti chinabuka pa sukulu ya pulayimale ya Chingale m'boma la Zomba pomwe ophunzira atatu adakomoka mosadziwika bwino Lachitatu m'mawa. Izi zitangochitika ...