Anthu okhala m'mudzi wa Chikho, Mfumu yayikulu Kasakula m'boma la Ntchisi adanduala za vuto la madzi lomwe lakula m'mudziwu. Mudzi wa Chikho mulibe dilawo komanso ...
M'modzi mwa yemwe akufuna kupikisana nawo pa mpando wa utsogoleri wa chipani cha United Transformation Movement (UTM), a Newtwon Kambala lero apereka zikalata ...
Chipwilikiti chinabuka pa sukulu ya pulayimale ya Chingale m'boma la Zomba pomwe ophunzira atatu adakomoka mosadziwika bwino Lachitatu m'mawa. Izi zitangochitika ...